MAYI KALIATI  CHONDE MUSAPANGE CHIWAWA | KU NTCHEWU  KWAFA KALE ANTHU ANAYI |

MAYI KALIATI CHONDE MUSAPANGE CHIWAWA | KU NTCHEWU KWAFA KALE ANTHU ANAYI |

DZIWE TV

4 месяца назад

20,725 Просмотров

Ссылки и html тэги не поддерживаются


Комментарии:

@JummaSAmick
@JummaSAmick - 16.06.2024 23:32

Mavuto plus mavuto

Ответить
@MelvinVanRooyen
@MelvinVanRooyen - 16.06.2024 23:36

Eeeeee nde zosayendatu

Ответить
@Amgwagwa
@Amgwagwa - 16.06.2024 23:38

Kwavuta kuntcheu

Ответить
@eunicesaiti
@eunicesaiti - 16.06.2024 23:45

Mizimu yawo iuse mu mtendere, MTSRIP😢😢😢😢

Ответить
@MsondaBanda
@MsondaBanda - 16.06.2024 23:51

Talk to UTM,

Ответить
@AlfredWalusa
@AlfredWalusa - 16.06.2024 23:56

Angoni ndiwokwiya zedi

Ответить
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj - 17.06.2024 00:00

AMALAWI SEGULANI MASSO SHONDE MR ASHANKWELA ANKOSA SHIWEMBU SHINASO SHOKUSA SIPHANI SINA SOSHUKA TIKALE SHELLU ANDU ANKUSIPE NKUMUKANI NOSE NKUPITA NKWA ASHANKWELA TETR HUWSSE ABWELLESE SHILIMA AWULURRE YENKA SOMWE WAPHANGA NGAT SAULULA ATULLE UDINDO PHASSI MOSATENGA 30DYS 💪💪💪💪 LIVE FROM PORT ELIZABETH SAUTH AFRICA

Ответить
@MaulanaomarKatundu
@MaulanaomarKatundu - 17.06.2024 00:10

A MCP wo bwanji sanafune kukambirana ndi Mr Chilima kungofikira kupha

Ответить
@adamyacinndawandawa4204
@adamyacinndawandawa4204 - 17.06.2024 00:25

Kufera zaeni

Ответить
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 - 17.06.2024 00:30

Sitikudabwa nazo coz kunanenedwa kuti akhesa magazi, lero siizi!, .

Ответить
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl - 17.06.2024 00:41

Ambuye titetezeni

Ответить
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl - 17.06.2024 00:41

Ambuye titetezeni

Ответить
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl - 17.06.2024 00:42

Tipemphere Malawi wathu

Ответить
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td - 17.06.2024 05:44

Aponyenso Maina Kaya tione convoy board yafa kapena UTM sapota penaso UTM amaonekanso Ngati ozindikira komaso ndiye mbuzi zawanthu akuthandizidwa but very stupid people including fuck readers otsala rubbish ndamene aphetse anthu Iwo azidya kwaoko kupusa Kwa anthu kumalora zautsiru akuumbuzani simunati do it

Ответить
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx - 17.06.2024 06:07

Chakwera wachita zopusa ndi cabinet yake kupha munthu osalakwa iyeyo asapite akaphedwako

Ответить
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx - 17.06.2024 06:13

Bata ngati alephela achakwerA pazomwe achita NDE bata INA ichokera kutu mutnthu anakuthandizani kuwina lelo kumupha chifujwachani tiphanaphana lelo

Ответить
@EnesrstMonda
@EnesrstMonda - 17.06.2024 06:42

Aaaaaa tikhare chete afawo ndi agaru anthu?

Ответить
@chikondiyovita7210
@chikondiyovita7210 - 17.06.2024 06:56

MAKHOKHODZANA,MAMUMULUDZA ndiso MABAYETE Akumva ululu Heavy Yagwayo ndi Mfumu yawo INKOSI BIYENI ONE. Wambawamba muona zidiyalamina Ndipakwo Mulungu yekha Odziwa Achitile chifundo pa Mtundu wa Amalawi Nzimuwawo Udekhe Chenene.

Ответить
@lutfieabrahams1465
@lutfieabrahams1465 - 17.06.2024 07:02

Ndpo anthuwa akutionjeza kwambili azingothipa ngati nkhuku choncho aaaaaa

Ответить
@TamaraWalaza
@TamaraWalaza - 17.06.2024 07:45

Imfayi zoonadi yawawa😢😢😢koma ena tikhale tcheru tifera za eni,nangah anthu afa 4 Aja Apita sabwereranso akuluakulu please stop confilct life is too short😢😢😢😢,akamabwerera chakwera anthu akufa musamale mutha kufa kudutsa pa 4samalan please!!!!!

Ответить
@MartinKapanga-q6m
@MartinKapanga-q6m - 17.06.2024 07:53

choyambilila choti muziwe ayamba kubweresa mpungwe mpungwe ndi apresdent aziko lamalawi pamodzi ndi asogoleli awo

Ответить
@MisheckAselo
@MisheckAselo - 17.06.2024 08:09

Mwapha biyeni dzikoli mukhale nalo 😭😭😭

Ответить
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri - 17.06.2024 08:20

Koma pena pake masapotafe sitikuganiza bwino, tawonani imfanzo sopano

Ответить
@rashidadan2533
@rashidadan2533 - 17.06.2024 08:31

Musayembekezele ubwino wa anthu , pomwe mwawuputa mkwiyo wawo

Ответить
@RaheemMogoya
@RaheemMogoya - 17.06.2024 08:31

Achakwela sanatiganizile bwino apanga zofuna iwowo

Ответить
@vytwistthelion98
@vytwistthelion98 - 17.06.2024 08:50

Olira sagwiridwa pakamwa forsek

Ответить
@GodisoneNoel
@GodisoneNoel - 17.06.2024 08:56

Anthu akufuna chakwera achoke ziwawa sizitha

Ответить
@PhillspicJere
@PhillspicJere - 17.06.2024 09:24

Kaliati ndiamene akulankhula ngati mwamuna, pamene mwamunayo akulankhula zopanda nzeru, Felix njawala ndiamene akukolezera ziwawa chifukwa cha zolankhula zake

Ответить
@marthaP-o2o
@marthaP-o2o - 17.06.2024 09:25

Kufa pa zinthu ngati izi si umbuli Koma kumankhala kumenyera ufulu dziko lanu FREEDOM IS COMING TOMORROW

Ответить
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g - 17.06.2024 09:25

Kaya zanu izo muziphana chocho ife prezideti wanthu ni boni karindo waanthu auphawi ife

Ответить
@WorriedNdhlovu
@WorriedNdhlovu - 17.06.2024 10:38

A mcp nawonso avala malaya a utm kut azisokoneza

Ответить
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw - 17.06.2024 12:56

Komatu zakwiyisa amalawi ambili zaifa yachilima

Ответить