Adzukulu ayika bokosi la maliro mu nyumba ya anfumu kamba kosapita nyama kumanda

Adzukulu ayika bokosi la maliro mu nyumba ya anfumu kamba kosapita nyama kumanda

Balanço semanal CK & Govate

2 месяца назад

5,406 Просмотров

Ссылки и html тэги не поддерживаются


Комментарии:

@obedFrancisKabokhoh
@obedFrancisKabokhoh - 10.10.2024 20:16

😢😢😢😢

Ответить
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin - 10.10.2024 20:18

Abale maliro sakomzekela pliz
Ndipo kukanakhala chilamulo choti nafedwa asamadyetse anthu
Anthu adzidya mmakwawo,
Malilo palibe yemwe amakomzekela😢😢😢😢😢😢

Ответить
@PetrosKambwera
@PetrosKambwera - 10.10.2024 20:18

Watching from PTA

Ответить
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 - 10.10.2024 20:24

Following sir

Ответить
@VictorireneuPio-d2n
@VictorireneuPio-d2n - 10.10.2024 20:27

Zovetsa chisoni kwambiri Moçambique wathu khaza zikuchuluka.

Ответить
@MisheckAselo
@MisheckAselo - 10.10.2024 20:28

Team Govate mumakwana watching from Lilongwe area 3

Ответить
@balancosemanalckgovate8464
@balancosemanalckgovate8464 - 10.10.2024 20:39

Onerani tsatane tsatane wa nkhani yonse

Ответить
@SiphokuhlePitar
@SiphokuhlePitar - 10.10.2024 20:49

Following you guys from sourth Africa but am from Malawi keep it up chibade may rest in peace

Ответить
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 - 10.10.2024 21:05

Nkhani yomvetsa chisoni kwambiri.Pakakhala vuto ndibwino kukambilana mwamtendere.

Ответить
@Indianaderick
@Indianaderick - 10.10.2024 21:16

Tizangophatikiza Mozambique nd Malawi 😂

Ответить
@Indianaderick
@Indianaderick - 10.10.2024 21:20

Anthu umunthu alibe like serious kupha zawo chfkwa cha magalas a mmaso? Really? Amangidwe amenewo

Ответить
@MadaritsoNgoma
@MadaritsoNgoma - 10.10.2024 22:07

Following you brother from South Africa but am from malawi

Ответить
@Odetta-e5n
@Odetta-e5n - 10.10.2024 22:12

Kulakwa abale kuchotsa moyo wamzathu

Ответить
@GeorgeKambwiri-xr9ri
@GeorgeKambwiri-xr9ri - 10.10.2024 22:54

Following you from south Africa original home Malawi

Ответить
@AnthonyPhiri-e3g
@AnthonyPhiri-e3g - 10.10.2024 23:12

Zambia Lusaka

Ответить
@DanJohn-ws5gl
@DanJohn-ws5gl - 10.10.2024 23:13

Watching you guys from Mangochi Malawi (zosaenda)komano Dela limenelo ndizaendelako kumachitika daily zodabwisa 😢😢😢

Ответить
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm - 10.10.2024 23:50

Govati mumakwana musamasowe, km kumozambiqu dziko lankhaza amakonda kuphana nkhan ya mowa

Ответить
@MalikiAlex-wn8jc
@MalikiAlex-wn8jc - 11.10.2024 00:19

Dj kamwana Mark 2 dedza boma zosakhalatu bwino

Ответить
@GiftgervásioGervásiolino
@GiftgervásioGervásiolino - 11.10.2024 00:23

Tete

Ответить
@AlinafeChimtengo
@AlinafeChimtengo - 11.10.2024 00:48

Tiripano

Ответить
@SoldierWilison
@SoldierWilison - 11.10.2024 02:17

Am from Malawi mangochi makanjira I love this channel BS channel and Bakili muluzi chaneel guys continue ndimakunyadila guys thanks ❤❤

Ответить
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj - 11.10.2024 06:24

Mulandu umenewo umayenera a police not afumu

Ответить
@austinvincent773
@austinvincent773 - 11.10.2024 08:10

Nyakwawayu ananenadi koma ithink anawalonjeza koma muchimowamowa

Ответить
@austinvincent773
@austinvincent773 - 11.10.2024 08:11

Ooooooo ndaivano mbuzi anyakwawa sanapatsidwe

Ответить
@Lameckbwanali-l3v
@Lameckbwanali-l3v - 11.10.2024 09:14

Koma a Mozambique muzipemphela mwanva but anyway agova ndi sizitu to the world

Ответить
@CatherineDesire
@CatherineDesire - 11.10.2024 09:28

Mmmmmh mmmmmh abare

Ответить
@RabeccaMwikho-f9h
@RabeccaMwikho-f9h - 11.10.2024 11:12

Kkkkkk mwinaso anyakwawawo analezela kkkkkk

Ответить
@AcácioAbrãoSinoia
@AcácioAbrãoSinoia - 11.10.2024 11:37

Mbambande timakunyadirani kwambili a Gova ndi a Cezito, komano nyakwawa kuthawa bokosi ???? Kakakakaka

Ответить
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev - 11.10.2024 15:20

Nyakwawa bibida anamupweteka mukanamutapa nkwikoso nyakwawayo

Ответить
@DanMdzinja
@DanMdzinja - 11.10.2024 18:44

Watching from Pretoria paboma penipeni anyakwawa mowa too much 😂😂😂😂

Ответить
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du - 12.10.2024 10:59

Zikoma govati pamozi ndi azanu pitilizani kutipasira mavidio koma mmmm zosayenda

Ответить
@Towexmpesi
@Towexmpesi - 12.10.2024 16:37

Am watching from Soweto

Ответить
@EnelessLangisoni
@EnelessLangisoni - 13.10.2024 22:23

😢😢😢😢ndisame kulakwa kwambili

Ответить